1 Samueli 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Samueli ananyamuka kuchoka ku Giligala kupita ku Gibeya wa ku Benjamini. Ndiyeno Sauli anawerenga anthu nʼkupeza kuti amene anatsala naye analipo amuna pafupifupi 600.+
15 Kenako Samueli ananyamuka kuchoka ku Giligala kupita ku Gibeya wa ku Benjamini. Ndiyeno Sauli anawerenga anthu nʼkupeza kuti amene anatsala naye analipo amuna pafupifupi 600.+