1 Samueli 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sauli, mwana wake Yonatani komanso anthu amene anatsala nawo aja ankakhala ku Geba+ wa ku Benjamini. Koma Afilisiti anali atamanga msasa ku Mikimasi.+
16 Sauli, mwana wake Yonatani komanso anthu amene anatsala nawo aja ankakhala ku Geba+ wa ku Benjamini. Koma Afilisiti anali atamanga msasa ku Mikimasi.+