-
1 Samueli 13:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Magulu atatu a asilikali ankabwera kuchokera mumsasa wa Afilisiti nʼkumalanda katundu. Gulu loyamba linkalowera kumsewu wopita ku Ofira, kudera la Suwali.
-