-
1 Samueli 13:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Mʼdziko lonse la Isiraeli munalibe wosula zitsulo. Izi zinali choncho chifukwa Afilisiti anati: “Kuti Aheberi asasule lupanga kapena mkondo.”
-