1 Samueli 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo pa tsiku lankhondo, pa anthu onse amene anali ndi Sauli ndi Yonatani panalibe aliyense amene anali ndi lupanga kapena mkondo.+ Sauli yekha ndi mwana wake Yonatani ndi amene anali ndi zida.
22 Ndipo pa tsiku lankhondo, pa anthu onse amene anali ndi Sauli ndi Yonatani panalibe aliyense amene anali ndi lupanga kapena mkondo.+ Sauli yekha ndi mwana wake Yonatani ndi amene anali ndi zida.