1 Samueli 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsiku lina Yonatani+ mwana wa Sauli anauza mtumiki wake yemwe ankamunyamulira zida kuti: “Tiye tipite patsidyapo kwa asilikali a Afilisiti.” Koma bambo ake sanawauze.
14 Tsiku lina Yonatani+ mwana wa Sauli anauza mtumiki wake yemwe ankamunyamulira zida kuti: “Tiye tipite patsidyapo kwa asilikali a Afilisiti.” Koma bambo ake sanawauze.