1 Samueli 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawiyi Sauli ankakhala kunja kwa mzinda wa Gibeya+ pansi pa mtengo wa makangaza* umene uli ku Migironi. Iye anali ndi anthu pafupifupi 600.+
2 Pa nthawiyi Sauli ankakhala kunja kwa mzinda wa Gibeya+ pansi pa mtengo wa makangaza* umene uli ku Migironi. Iye anali ndi anthu pafupifupi 600.+