-
1 Samueli 14:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Pakati pa mipata imene Yonatani ankafuna kudutsa kuti akamenyane ndi asilikali a Afilisiti, panali matanthwe awiri. Lililonse linkaoneka ngati dzino ndipo lina linali mbali ina, lina mbali ina. Mayina a matanthwewo anali Bozezi ndi Sene.
-