1 Samueli 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Yonatani anauza womunyamulira zida uja kuti: “Tiye tipite kwa amuna osadulidwawa.+ Mwina Yehova adzatithandiza, chifukwa palibe chimene chingalepheretse Yehova kupulumutsa pogwiritsa ntchito anthu ambiri kapena ochepa.”+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:6 Nsanja ya Olonda,1/1/1989, tsa. 24
6 Choncho Yonatani anauza womunyamulira zida uja kuti: “Tiye tipite kwa amuna osadulidwawa.+ Mwina Yehova adzatithandiza, chifukwa palibe chimene chingalepheretse Yehova kupulumutsa pogwiritsa ntchito anthu ambiri kapena ochepa.”+