1 Samueli 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma akakatiuza kuti, ‘Bwerani mudzamenyane nafe!’ ife tikapitedi chifukwa Yehova akawapereka mʼmanja mwathu. Chimenechi chidzakhala chizindikiro chathu.”+
10 Koma akakatiuza kuti, ‘Bwerani mudzamenyane nafe!’ ife tikapitedi chifukwa Yehova akawapereka mʼmanja mwathu. Chimenechi chidzakhala chizindikiro chathu.”+