1 Samueli 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo iwo anachita zoti asilikali a Afilisiti awaone. Afilisitiwo atawaona anati: “Taonani Aheberi akutuluka mʼmaenje amene anabisala.”+
11 Ndipo iwo anachita zoti asilikali a Afilisiti awaone. Afilisitiwo atawaona anati: “Taonani Aheberi akutuluka mʼmaenje amene anabisala.”+