-
1 Samueli 14:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndiyeno Yonatani anakwera matanthwe chokwawa ndipo mtumiki wake ankabwera mʼmbuyo mwake. Kenako Yonatani anayamba kupha Afilisitiwo ndipo mtumiki wake uja ankamalizitsa aliyense amene sanafe.
-