1 Samueli 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zitatero Sauli anauza Ahiya+ kuti: “Bweretsa kuno Likasa la Mulungu woona!” (Pa nthawiyi nʼkuti Likasa la Mulungu woona lili ndi Aisiraeli.)
18 Zitatero Sauli anauza Ahiya+ kuti: “Bweretsa kuno Likasa la Mulungu woona!” (Pa nthawiyi nʼkuti Likasa la Mulungu woona lili ndi Aisiraeli.)