-
1 Samueli 14:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Komanso Aheberi amene poyamba anagwirizana ndi Afilisiti, ndipo anapita kukakhala mumsasa wa Afilisiti, anachoka nʼkupita kumbali ya Aisiraeli amene anali ndi Sauli ndi Yonatani.
-