1 Samueli 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Amuna onse a Isiraeli amene anabisala+ mʼdera lamapiri la Efuraimu anamva kuti Afilisiti akuthawa, choncho nawonso anayamba kuthamangitsa Afilisitiwo.
22 Amuna onse a Isiraeli amene anabisala+ mʼdera lamapiri la Efuraimu anamva kuti Afilisiti akuthawa, choncho nawonso anayamba kuthamangitsa Afilisitiwo.