24 Koma amuna a Isiraeli anatopa kwambiri pa tsikuli chifukwa Sauli analumbirira anthuwo kuti: “Munthu aliyense amene angadye chakudya chilichonse dzuwa lisanalowe, komanso ndisanabwezere adani anga, akhale wotembereredwa.” Choncho panalibe aliyense amene anadya chilichonse.+