1 Samueli 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pa tsikuli iwo anapitiriza kupha Afilisiti kuyambira ku Mikimasi mpaka ku Aijaloni+ ndipo anthu anatopa kwambiri.
31 Pa tsikuli iwo anapitiriza kupha Afilisiti kuyambira ku Mikimasi mpaka ku Aijaloni+ ndipo anthu anatopa kwambiri.