1 Samueli 14:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Zitatero, anthuwo anayamba kuthamangira zinthu za adani awowo mosusuka ndipo anatenga nkhosa, ngʼombe ndi ana a ngʼombe. Ankaziphera pansi ndipo ankadya nyamayo pamodzi ndi magazi ake.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:32 Nsanja ya Olonda,4/15/1994, tsa. 31
32 Zitatero, anthuwo anayamba kuthamangira zinthu za adani awowo mosusuka ndipo anatenga nkhosa, ngʼombe ndi ana a ngʼombe. Ankaziphera pansi ndipo ankadya nyamayo pamodzi ndi magazi ake.+