1 Samueli 14:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndiyeno Sauli anamangira Yehova guwa lansembe.+ Limeneli linali guwa lake loyamba kumangira Yehova.
35 Ndiyeno Sauli anamangira Yehova guwa lansembe.+ Limeneli linali guwa lake loyamba kumangira Yehova.