-
1 Samueli 14:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo, amene anapulumutsa Aisiraeli, yemwe wachita tchimoli ayenera kufa, ngakhale atakhala Yonatani mwana wanga.” Koma palibe aliyense amene anamuyankha.
-