1 Samueli 14:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Sauli anafunsa Yonatani kuti: “Ndiuze, wachita chiyani?” Yonatani anayankha kuti: “Ndinalawa uchi pangʼono kunsonga ya ndodo imene ndatengayi.+ Ndiye ndine ndili pano. Mukhoza kundipha!”
43 Sauli anafunsa Yonatani kuti: “Ndiuze, wachita chiyani?” Yonatani anayankha kuti: “Ndinalawa uchi pangʼono kunsonga ya ndodo imene ndatengayi.+ Ndiye ndine ndili pano. Mukhoza kundipha!”