-
1 Samueli 14:45Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
45 Koma anthu anauza Sauli kuti: “Kodi Yonatani amene wapulumutsa+ Aisiraeli chonchi afe? Sizitheka zimenezo! Tikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo, ngakhale tsitsi limodzi la mʼmutu wake siligwa pansi, chifukwa zimene wachita lerozi wathandizidwa ndi Mulungu.”+ Ndi mawu amenewa anthuwo anapulumutsa* Yonatani moti sanaphedwe.
-