1 Samueli 14:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Iye ankamenya nkhondo molimba mtima ndipo anagonjetsa Aamaleki+ nʼkupulumutsa Aisiraeli kwa adani awowo.
48 Iye ankamenya nkhondo molimba mtima ndipo anagonjetsa Aamaleki+ nʼkupulumutsa Aisiraeli kwa adani awowo.