1 Samueli 14:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ana aamuna a Sauli anali Yonatani, Isivi ndi Malikisuwa.+ Iye analinso ndi ana aakazi awiri. Wamkulu dzina lake anali Merabu+ pamene wamngʼono anali Mikala.+
49 Ana aamuna a Sauli anali Yonatani, Isivi ndi Malikisuwa.+ Iye analinso ndi ana aakazi awiri. Wamkulu dzina lake anali Merabu+ pamene wamngʼono anali Mikala.+