1 Samueli 14:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Mkazi wa Sauli dzina lake anali Ahinowamu, mwana wa Ahimazi. Mkulu wa gulu lake lankhondo anali Abineri+ mwana wa Nera, mchimwene wawo wa bambo ake a Sauli.
50 Mkazi wa Sauli dzina lake anali Ahinowamu, mwana wa Ahimazi. Mkulu wa gulu lake lankhondo anali Abineri+ mwana wa Nera, mchimwene wawo wa bambo ake a Sauli.