1 Samueli 14:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Bambo ake a Sauli anali Kisi,+ ndipo Nera+ bambo ake a Abineri, anali mwana wa Abiyeli.