1 Samueli 14:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Sauli ankamenyana kwambiri ndi Afilisiti mʼmasiku onse a moyo wake.+ Ndipo Sauli ankati akaona munthu aliyense wamphamvu kapena wolimba mtima, ankamutenga kuti akhale msilikali wake.+
52 Sauli ankamenyana kwambiri ndi Afilisiti mʼmasiku onse a moyo wake.+ Ndipo Sauli ankati akaona munthu aliyense wamphamvu kapena wolimba mtima, ankamutenga kuti akhale msilikali wake.+