1 Samueli 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Sauli ndi anthu ake anasiya* Agagi, nkhosa ndi ngʼombe zabwino kwambiri, ziweto zonenepa, nkhosa zamphongo ndi zina zonse zimene zinali zabwino.+ Iwo sanafune kupha zimenezi, koma zinthu zonse zimene zinali zachabechabe ndi zosafunika anaziwononga.
9 Sauli ndi anthu ake anasiya* Agagi, nkhosa ndi ngʼombe zabwino kwambiri, ziweto zonenepa, nkhosa zamphongo ndi zina zonse zimene zinali zabwino.+ Iwo sanafune kupha zimenezi, koma zinthu zonse zimene zinali zachabechabe ndi zosafunika anaziwononga.