1 Samueli 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ndikumva chisoni kuti ndinaika Sauli kukhala mfumu. Iye wasiya kunditsatira, ndipo sanamvere mawu anga.”+ Samueli anakhumudwa kwambiri ndi nkhaniyi moti analirira Yehova usiku wonse.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:11 Nsanja ya Olonda,4/15/1998, ptsa. 6-7
11 “Ndikumva chisoni kuti ndinaika Sauli kukhala mfumu. Iye wasiya kunditsatira, ndipo sanamvere mawu anga.”+ Samueli anakhumudwa kwambiri ndi nkhaniyi moti analirira Yehova usiku wonse.+