-
1 Samueli 15:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Patapita nthawi Samueli anamʼpeza Sauli, ndipo Sauli anauza Samueli kuti: “Yehova akudalitseni. Ndachita zimene Yehova ananena.”
-