1 Samueli 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma Samueli anati: “Akazi anaferedwa ana awo chifukwa cha lupanga lako, choncho mayi akonso aferedwa kuposa akazi onse.” Kenako Samueli anadula Agagi mapisimapisi pamaso pa Yehova ku Giligala.+
33 Koma Samueli anati: “Akazi anaferedwa ana awo chifukwa cha lupanga lako, choncho mayi akonso aferedwa kuposa akazi onse.” Kenako Samueli anadula Agagi mapisimapisi pamaso pa Yehova ku Giligala.+