1 Samueli 15:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Samueli analirira Sauli ndipo sanaonanenso naye mpaka tsiku limene Samueliyo anamwalira.+ Yehova anamva chisoni kuti anaika Sauli kukhala mfumu ya Isiraeli.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:35 Nsanja ya Olonda,4/15/1998, ptsa. 6-7
35 Samueli analirira Sauli ndipo sanaonanenso naye mpaka tsiku limene Samueliyo anamwalira.+ Yehova anamva chisoni kuti anaika Sauli kukhala mfumu ya Isiraeli.+