1 Samueli 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno ukaitanire Jese kopereka nsembeko, ndipo ine ndidzakuuza zochita. Ukandidzozere munthu amene ndidzakusonyeza.”+
3 Ndiyeno ukaitanire Jese kopereka nsembeko, ndipo ine ndidzakuuza zochita. Ukandidzozere munthu amene ndidzakusonyeza.”+