1 Samueli 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Samueli anachita zimene Yehova anamuuza. Atafika ku Betelehemu,+ akulu a mzindawo anayamba kunjenjemera atakumana naye ndipo anamufunsa kuti: “Kodi nʼkwabwino?”
4 Samueli anachita zimene Yehova anamuuza. Atafika ku Betelehemu,+ akulu a mzindawo anayamba kunjenjemera atakumana naye ndipo anamufunsa kuti: “Kodi nʼkwabwino?”