1 Samueli 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Yehova anauza Samueli kuti: “Usaganizire mmene akuonekera komanso kutalika kwake+ chifukwa ine ndamukana ameneyu. Chifukwatu mmene munthu amaonera si mmene Mulungu amaonera. Munthu amaona zooneka ndi maso, koma Yehova amaona mumtima.”+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:7 Nsanja ya Olonda,3/1/2010, tsa. 2311/15/2004, tsa. 203/15/2003, tsa. 156/15/1999, tsa. 2211/1/1989, tsa. 28
7 Koma Yehova anauza Samueli kuti: “Usaganizire mmene akuonekera komanso kutalika kwake+ chifukwa ine ndamukana ameneyu. Chifukwatu mmene munthu amaonera si mmene Mulungu amaonera. Munthu amaona zooneka ndi maso, koma Yehova amaona mumtima.”+
16:7 Nsanja ya Olonda,3/1/2010, tsa. 2311/15/2004, tsa. 203/15/2003, tsa. 156/15/1999, tsa. 2211/1/1989, tsa. 28