1 Samueli 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Samueli anatenga nyanga ya mafuta+ nʼkumudzoza azichimwene ake akuona. Kuyambira tsiku limenelo, mzimu wa Yehova unayamba kuthandiza Davide.+ Kenako Samueli anabwerera ku Rama.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:13 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 5 2016, tsa. 9
13 Samueli anatenga nyanga ya mafuta+ nʼkumudzoza azichimwene ake akuona. Kuyambira tsiku limenelo, mzimu wa Yehova unayamba kuthandiza Davide.+ Kenako Samueli anabwerera ku Rama.+