1 Samueli 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mbuye wathu, uzani atumiki anu kuti akupezereni katswiri woimba zeze.+ Mzimu woipa wochokera kwa Mulungu ukakubwererani, iye azikuimbirani zeze ndipo inu muzimva bwino.”
16 Mbuye wathu, uzani atumiki anu kuti akupezereni katswiri woimba zeze.+ Mzimu woipa wochokera kwa Mulungu ukakubwererani, iye azikuimbirani zeze ndipo inu muzimva bwino.”