-
1 Samueli 16:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Choncho Sauli anauza atumiki ake kuti: “Ndipezereni munthu wodziwa kuimba, ndipo mubwere naye kuno.”