1 Samueli 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mmodzi wa atumikiwo ananena kuti: “Ine ndinaona mwana wa Jese wa ku Betelehemu akuimba, ndipo amaimba mwaluso. Iye ndi mwamuna wolimba mtima ndiponso msilikali wamphamvu.+ Ndiwodziwa kulankhula, wooneka bwino+ komanso Yehova ali naye.”+
18 Mmodzi wa atumikiwo ananena kuti: “Ine ndinaona mwana wa Jese wa ku Betelehemu akuimba, ndipo amaimba mwaluso. Iye ndi mwamuna wolimba mtima ndiponso msilikali wamphamvu.+ Ndiwodziwa kulankhula, wooneka bwino+ komanso Yehova ali naye.”+