1 Samueli 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Sauli atamva zimenezi, anatumiza uthenga kwa Jese wakuti: “Nditumizire mwana wako Davide amene amaweta nkhosa.”+
19 Sauli atamva zimenezi, anatumiza uthenga kwa Jese wakuti: “Nditumizire mwana wako Davide amene amaweta nkhosa.”+