-
1 Samueli 16:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Choncho Jese anatenga mkate, thumba lachikopa la vinyo ndi mwana wa mbuzi nʼkuziika pa bulu kuti mwana wake Davide apite nazo kwa Sauli.
-