1 Samueli 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno maganizo oipa* akamubwerera Sauli, Davide ankatenga zeze nʼkumuimbira. Akatero, Sauli ankamva bwino ndipo maganizo oipawo ankamuchokera.+
23 Ndiyeno maganizo oipa* akamubwerera Sauli, Davide ankatenga zeze nʼkumuimbira. Akatero, Sauli ankamva bwino ndipo maganizo oipawo ankamuchokera.+