1 Samueli 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Sauli ndi asilikali a Isiraeli anasonkhana nʼkumanga msasa mʼchigwa cha Ela,+ ndipo anakonzeka kuti amenyane ndi Afilisiti. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:2 ‘Dziko Lokoma’, tsa. 16
2 Sauli ndi asilikali a Isiraeli anasonkhana nʼkumanga msasa mʼchigwa cha Ela,+ ndipo anakonzeka kuti amenyane ndi Afilisiti.