1 Samueli 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anavalanso zoteteza miyendo zakopa komanso anakolekera nthungo+ yakopa kumsana kwake.