1 Samueli 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mtengo wa mkondo wake unali waukulu ngati mtengo wogwiritsa ntchito powomba nsalu,+ ndipo mutu wachitsulo wa mkondowo unali wolemera makilogalamu pafupifupi 7.* Munthu womunyamulira chishango chake ankayenda patsogolo pake. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:7 Nsanja ya Olonda,5/15/2006, tsa. 91/1/1989, ptsa. 18-19
7 Mtengo wa mkondo wake unali waukulu ngati mtengo wogwiritsa ntchito powomba nsalu,+ ndipo mutu wachitsulo wa mkondowo unali wolemera makilogalamu pafupifupi 7.* Munthu womunyamulira chishango chake ankayenda patsogolo pake.