-
1 Samueli 17:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ngati angathe kumenyana nane nʼkundipha, ndiye kuti tidzakhala antchito anu. Koma ngati ndingamugonjetse mpaka kumupha, inuyo mudzakhala antchito athu ndipo muzititumikira.”
-