1 Samueli 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana atatu aakulu a Jese anapita ndi Sauli kunkhondo.+ Woyamba kubadwa dzina lake anali Eliyabu,+ wachiwiri anali Abinadabu+ ndipo wachitatu anali Shama.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:13 Nsanja ya Olonda,9/1/2011, tsa. 29
13 Ana atatu aakulu a Jese anapita ndi Sauli kunkhondo.+ Woyamba kubadwa dzina lake anali Eliyabu,+ wachiwiri anali Abinadabu+ ndipo wachitatu anali Shama.+