1 Samueli 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Davide anali wamngʼono kwambiri+ pa onse ndipo ana atatu aakulu a Jese anatsatira Sauli.