1 Samueli 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Utengenso mapisi 10 awa a tchizi* ukapatse mtsogoleri wa gulu la anthu 1,000. Ukafufuzenso kuti azichimwene ako ali bwanji, ndipo akakupatse chizindikiro chosonyeza kuti ali bwino.”
18 Utengenso mapisi 10 awa a tchizi* ukapatse mtsogoleri wa gulu la anthu 1,000. Ukafufuzenso kuti azichimwene ako ali bwanji, ndipo akakupatse chizindikiro chosonyeza kuti ali bwino.”