-
1 Samueli 17:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Choncho Davide anadzuka mʼmamawa ndipo nkhosa zake anasiyira munthu wina. Iye analongedza katundu wake nʼkunyamuka mogwirizana ndi zimene bambo ake anamuuza. Atafika mumsasa, anapeza asilikali akupita kumalo omenyera nkhondo kwinaku akufuula.
-